Ezekieli 23:19 BL92

19 Koma anacurukitsa zigololo zace, nakumbukila masiku a ubwana wace, muja anacita cigololo m'dziko la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23

Onani Ezekieli 23:19 nkhani