45 Ndipo anthu olungama adzawaweruza monga mwa maweruzo a acigololo, ndi maweruzo a akazi okhetsa mwazi; pakuti ndiwo acigololo, ndi m'manja mwao muli mwazi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:45 nkhani