Ezekieli 23:46 BL92

46 Pakuti atero Ambuye Yehova, Ndidzawakweretsera msonkhano wa anthu, ndi kuwapereka awazunze, ndi kulanda cuma cao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23

Onani Ezekieli 23:46 nkhani