Ezekieli 24:5 BL92

5 Tengako coweta cosankhika, nuikire mafupa mulu wa nkhuni pansi; ubwadamuke, ndi mafupa ace omwe uwaphike m'mwemo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24

Onani Ezekieli 24:5 nkhani