Ezekieli 24:6 BL92

6 Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Tsoka mudzi wokhetsa mwazi, mphika m'mene muli dzimbiri, losaucokera dzimbiri lace; ucotsemo ciwalo ciwalo; sanaugwera maere.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24

Onani Ezekieli 24:6 nkhani