Ezekieli 25:10 BL92

10 kuwapereka kwa ana a kum'mawa pamodzi ndi ana a Amoni; ndipo ndidzawapereka akhale ao ao, kuti ana a Amoni asakumbukikenso mwa amitundu;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 25

Onani Ezekieli 25:10 nkhani