Ezekieli 25:9 BL92

9 cifukwa cace taona, ndidzatsegula pambali pace pa Moabu kuyambira ku midzi, ku midzi yace yokhala mphepete, yokometsetsa ya m'dziko, Betiyesimoti, Baalameoni, ndi Kiriataimu,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 25

Onani Ezekieli 25:9 nkhani