Ezekieli 25:5 BL92

5 Ndipo ndidzayesa Raba khola la ngamira, ndi ana a Amoni popumula zoweta zazing'ono; matero mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 25

Onani Ezekieli 25:5 nkhani