Ezekieli 27:16 BL92

16 Aramu anacita nawe malonda cifukwa ca zambirizo udazipanga, anagula malonda ako ndi smaragido, nsaru yofiirira, ndi yopikapika, ndi bafuta, ndi korale, ndi ngale.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:16 nkhani