Ezekieli 27:17 BL92

17 Yuda ndi dziko la Israyeli anagulana nawe malonda, anagula malonda ako ndi tirigu wa ku Miniti, ndi zozuna, ndi uci, ndi mafuta, ndi mafuta amankhwala.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:17 nkhani