22 Amalonda a ku Seba ndi a ku Rama anagulana nawe malonda; anagula malonda ako ndi zonunkhira zoposa ziri zonse, ndi miyala iri yonse ya mtengo wace, ndi golidi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27
Onani Ezekieli 27:22 nkhani