Ezekieli 27:24 BL92

24 Awa anagulana nawe malonda ndi zobvala zosankhika, ndi mitumba ya nsaru zofiirira ndi zopikapika, ndi cuma ca thonje lopotapota, ndi zingwe zopota zolimba za malonda ako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:24 nkhani