Ezekieli 27:25 BL92

25 Zombo za ku Tarisi ndizo amtengatenga a malonda ako; ndipo unadzazidwa ndi cuma ndi ulemu waukuru pakati pa nyanja,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:25 nkhani