Ezekieli 27:32 BL92

32 Ndipo pakulira adzakukwezera nyimbo ya maliro, ndi kukulirira, ndi kuti, Wakunga Turo ndani, wakunga uyu waonongeka pakati pa nyanja?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:32 nkhani