Ezekieli 27:33 BL92

33 Pakuturuka malonda ako m'nyanja unadzaza mitundu yambiri ya anthu, unalemeretsa mafumu a pa dziko lapansi ndi cuma cako cocuruka ndi malonda ako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:33 nkhani