23 Pakuti ndidzatumiza mliri ndi mwazi ilowe m'makwalala ace, ndi olasidwa adzagwa m'kati mwace ndi lupanga lougwera pozungulira ponse; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28
Onani Ezekieli 28:23 nkhani