Ezekieli 28:24 BL92

24 Ndipo nyumba ya Israyeli siidzakhalanso nayo mitungwi yolasa, kapena minga yaululu ya ali yense wakuizinga ndi kuipeputsa; motero adzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28

Onani Ezekieli 28:24 nkhani