Ezekieli 29:10 BL92

10 Cifukwa cace taona, nditsutsana ndi iwe ndi mitsinje yako, ndipo ndidzasandutsa dziko la Aigupto likhale lopasuka konse, ndi labwinja, kuyambira nsanja ya Sevene kufikira malire a Kusi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29

Onani Ezekieli 29:10 nkhani