9 Ndi dziko la Aigupto lidzakhala lopasuka ndi labwinja; ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, popeza anati, Mtsinjewo ndi wanga, ndinaulenga ndine.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29
Onani Ezekieli 29:9 nkhani