Ezekieli 29:15 BL92

15 Udzakhala wopepuka wa maufumu onse, sudzadzikwezanso pa amitundu; ndipo ndidzawacepsa, kuti asacitenso ufumu pa amitundu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29

Onani Ezekieli 29:15 nkhani