Ezekieli 29:16 BL92

16 Ndipo sudzakhalanso cotama ca nyumba ya Israyeli, kukumbutsa mphulupulu, pakuwatembenukira kuwatsata; motero adzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29

Onani Ezekieli 29:16 nkhani