Ezekieli 29:6 BL92

6 Ndi onse okhala m'Aigupto adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, popeza anakhalira nyumba ya Israyeli mcirikizo wabango.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29

Onani Ezekieli 29:6 nkhani