Ezekieli 3:10 BL92

10 Ananenanso nane, Wobadwa ndi munthu iwe, mau anga onse ndidzawanena ndi iwe uwalandire m'mtima mwako, utawamva m'makutu mwako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:10 nkhani