Ezekieli 3:9 BL92

9 Ndalimbitsa mutu wako woposa mwala wolimbitsitsa, usawaopa kapena kutenga nkhawa pamaso pao; pakuti iwo ndiwo nyumba yopanduka.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:9 nkhani