17 Wobadwa ndi munthu iwe, ndakuika ukhale mlonda wa nyumba ya Israyeli, m'mwemo mvera mau oturuka m'kamwa mwanga, nundicenjezere iwo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3
Onani Ezekieli 3:17 nkhani