21 Koma ukamcenjeza wolungamayo, kuti asacimwe wolungamayo, ndipo sacimwa, adzakhala ndi moyo ndithu, popeza anacenjezedwa; ndipo iwe walanditsa moyo wako.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3
Onani Ezekieli 3:21 nkhani