Ezekieli 3:22 BL92

22 Ndipo dzanja la Yehova linandikhalira komweko, nati kwa ine, Nyamuka, turuka kumka kucidikha, ndipo pomwepo ndidzalankhula ndi iwe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:22 nkhani