Ezekieli 3:6 BL92

6 si kwa mitundu yambiri ya anthu a cinenedwe cosamveka ndi cobvuta, amene sukhoza kudziwitsa cinenedwe cao. Zedi ndikakutumiza kwa iwowa adzamvera iwe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:6 nkhani