Ezekieli 3:7 BL92

7 Koma nyumba ya Israyeli siidzakumvera, pakuti siifuna kundimvera Ine; pakuti nyumba yonse ya Israyeli ndiyo yolimba mutu ndi youma mtima.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:7 nkhani