Ezekieli 30:7 BL92

7 Ndipo adzakhala opasuka pakati pa maiko opasuka, ndi midzi yace idzakhala pakati pa midzi yopasuka.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 30

Onani Ezekieli 30:7 nkhani