14 Pamenepo ndidzadikhitsa madzi ace, ndi kuyendetsa madzi a m'mitsinje mwao ngati mafuta, ati Ambuye Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32
Onani Ezekieli 32:14 nkhani