15 Pakusanduliza Ine dziko la Aigupto likhale lopasuka ndi labwinja, dziko losowa zodzaza zace, pakukantha Ine onse okhala m'mwemo, pamenepo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32
Onani Ezekieli 32:15 nkhani