16 Iyi ndi nyimbo ya maliro adzalira nayo, ana akazi a amitundu adzacita nayo maliro; adzalirira nayo Aigupto ndi aunyinji ace onse, ati Ambuye Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32
Onani Ezekieli 32:16 nkhani