Ezekieli 33:30 BL92

30 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, ana a anthu a mtundu wako anena za iwe ku makoma ndi ku makomo a nyumba zao, nanenana yense ndi mbale wace, ndi kuti, Tiyeni tikamve mau ofuma kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33

Onani Ezekieli 33:30 nkhani