31 Ndipo akudzera monga amadzera anthu, nakhala pansi pamaso pako ngati anthu anga, namva mau ako, koma osawacita; pakuti pakamwa pao anena mwacikondi, koma mtima wao utsata phindu lao.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33
Onani Ezekieli 33:31 nkhani