32 Ndipo taona, akuyesa iwe ngati nyimbo yacikondi ya woyimba bwino, woyimba limba bwino; pakuti akumva mau ako, koma osawacita.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33
Onani Ezekieli 33:32 nkhani