9 Koma ukacenjeza woipa za njira yace, aileke; koma iye osaileka njira yace, adzafa m'mphulupulu mwace iye, koma iwe walanditsa moyo wako.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33
Onani Ezekieli 33:9 nkhani