Ezekieli 33:8 BL92

8 Ndikati Ine kwa woipa, Woipawe, udzafa ndithu, osanena iwe kumcenjeza woipayo aleke njira yace, woipa uyo adzafa m'mphulupulu yace, koma mwazi wace ndidzaufunsa pa dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33

Onani Ezekieli 33:8 nkhani