Ezekieli 33:7 BL92

7 Iwe tsono, wobadwa ndi munthu, ndakuika mlonda wa nyumba ya Israyeli, m'mwemo imva mau a pakamwa panga, nundicenjezere iwo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33

Onani Ezekieli 33:7 nkhani