14 Ndidzazidyetsa podyetsa pabwino; ndi pa mapiri atali a Israyeli padzakhala kholo lao, apo adzagona m'khola mwabwino, nadzadya podyetsa pokometsetsa pa mapiri a Israyeli.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34
Onani Ezekieli 34:14 nkhani