Ezekieli 34:28 BL92

28 Ndipo sadzakhalanso cakudya ca amitundu, ndi cirombo ca kuthengo sicidzawadyanso; koma adzakhala osatekeseka, opanda wina wakuwaopsa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:28 nkhani