Ezekieli 34:30 BL92

30 Ndipo adzadziwa kuti Ine Yehova Mulungu wao ndiri nao, ndi kuti iwo, nyumba ya Israyeli, ndiwo anthu anga, ati Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:30 nkhani