Ezekieli 34:31 BL92

31 Ndipo inu nkhosa zanga, nkhosa za pabusa panga, ndinu anthu, ndi Ine ndine Mulungu wanu, ati Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:31 nkhani