10 Popeza wanena, Mitundu iwiri iyi ya anthu ndi maiko awiri awa adzakhala anga, tidzakhala nao ngati colowa cathu, angakhale Yehova anali komweko;
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 35
Onani Ezekieli 35:10 nkhani