Ezekieli 35:11 BL92

11 cifukwa cace, Pali Ine, ati Ambuye Yehova, ndidzacita monga mwa mkwiyo wako, ndi monga mwa nsanje yako unacita nayo pa kukwiya nao iwe; ndipo ndidzadziwika nao pamene ndikuweruza.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 35

Onani Ezekieli 35:11 nkhani