Ezekieli 35:12 BL92

12 Ndipo udzadziwa kuti Ine Yehova ndidamva zamwano zako zonse udazinena pa mapiri a Israyeli, ndi kuti, Apasuka, apatsidwa kwa ife tiwadye.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 35

Onani Ezekieli 35:12 nkhani