1 Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, unenere kwa mapiri a Israyeli, uziti, Mapiri a Israyeli inu, imvani mau a Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36
Onani Ezekieli 36:1 nkhani