Ezekieli 36:17 BL92

17 Wobadwa ndi munthu iwe, muja a nyumba ya Israyeli anakhala m'dziko mwao, analidetsa ndi njira yao, ndi macitidwe ao; njira yao pamaso panga inanga cidetso ca mkazi wooloka.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:17 nkhani