18 M'mwemo ndinawatsanulira ukali wanga, cifukwa ca mwazi anautsanulira padziko, ndi cifukwa ca mafano analidetsa dziko nao;
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36
Onani Ezekieli 36:18 nkhani