Ezekieli 36:19 BL92

19 ndipo ndinawabalalitsa mwa amitundu, namwazika m'maiko monga mwa njira yao; ndi monga mwa macitidwe ao ndinawaweruza.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 36

Onani Ezekieli 36:19 nkhani